Mfumu ya mafumu inadza kwa anthu ake, Aisrayeli, m’cholowa chake, koma anthu ake sanamlandire. Iye akusiya chisoti chake chachifumu pamodzi ndi Atate wake kuti adziveke pa iye yekha korona wa minga: “Asilikali analuka chisoti chachifumu chaminga, nachiveka pamutu pake, nambveka iye mwinjiro wa chibakuwa, nadza kwa iye, nati. , Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda ! Ndipo anamumenya iye kumaso.” ( Yoh9,2-3). Yesu adzilola yekha...
Werengani zambiri ➜